1 Mbiri 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Merari anali Mali ndi Musi. Mabanja a Alevi potsatira mayina a makolo awo anali awa:+