1 Mbiri 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwana wa Kohati anali Aminadabu, mwana wa Aminadabu anali Kora,+ mwana wa Kora anali Asiri,