1 Mbiri 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Awa ndi anthu amene Davide anawapatsa udindo wotsogolera kuimba panyumba ya Yehova ataikapo Likasa.+
31 Awa ndi anthu amene Davide anawapatsa udindo wotsogolera kuimba panyumba ya Yehova ataikapo Likasa.+