1 Mbiri 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Awa ndi amene ankatumikira limodzi ndi ana awo: Anthu a mʼbanja la Kohati, Hemani+ woimba, mwana wa Yoweli.+ Yoweli anali mwana wa Samueli,
33 Awa ndi amene ankatumikira limodzi ndi ana awo: Anthu a mʼbanja la Kohati, Hemani+ woimba, mwana wa Yoweli.+ Yoweli anali mwana wa Samueli,