1 Mbiri 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Abale awo ena, omwe anali mbadwa za Merari,+ ankakhala kumanzere. Panali Etani+ mwana wa Kisa. Kisa anali mwana wa Abidi, Abidi anali mwana wa Maluki,
44 Abale awo ena, omwe anali mbadwa za Merari,+ ankakhala kumanzere. Panali Etani+ mwana wa Kisa. Kisa anali mwana wa Abidi, Abidi anali mwana wa Maluki,