1 Mbiri 6:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Abale awo, Alevi, anasankhidwa kuti azichita utumiki wonse wapachihema chopatulika, chomwe chinali nyumba ya Mulungu woona.+
48 Abale awo, Alevi, anasankhidwa kuti azichita utumiki wonse wapachihema chopatulika, chomwe chinali nyumba ya Mulungu woona.+