1 Mbiri 6:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Anapatsidwa mzinda wa Heburoni+ mʼdziko la Yuda ndi malo odyetserako ziweto ozungulira mzindawo.