1 Mbiri 6:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Anthu a mʼbanja la Gerisomu, potsatira mabanja awo, anawapatsa mizinda 13 kuchokera ku fuko la Isakara, fuko la Aseri, fuko la Nafitali ndi fuko la Manase ku Basana.+
62 Anthu a mʼbanja la Gerisomu, potsatira mabanja awo, anawapatsa mizinda 13 kuchokera ku fuko la Isakara, fuko la Aseri, fuko la Nafitali ndi fuko la Manase ku Basana.+