1 Mbiri 6:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Anthu a mʼbanja la Merari, potsatira mabanja awo, anawapatsa mizinda 12 kuchokera ku fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi fuko la Zebuloni.+
63 Anthu a mʼbanja la Merari, potsatira mabanja awo, anawapatsa mizinda 12 kuchokera ku fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi fuko la Zebuloni.+