-
1 Mbiri 6:65Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
65 Komanso, atachita maere anawapatsa mizinda imeneyi kuchokera ku fuko la Yuda, fuko la Simiyoni ndi fuko la Benjamini. Mizindayo anachita kuitchula mayina.
-