1 Mbiri 6:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Anawapatsa mzinda wothawirako wa Sekemu+ ndi malo ake odyetserako ziweto kudera lamapiri la Efuraimu, mzinda wa Gezeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
67 Anawapatsa mzinda wothawirako wa Sekemu+ ndi malo ake odyetserako ziweto kudera lamapiri la Efuraimu, mzinda wa Gezeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto,