1 Mbiri 6:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Kuchokera ku banja la hafu ya fuko la Manase, anapatsa anthu a ku banja la Gerisomu mzinda wa Golani+ ku Basana ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Asitaroti ndi malo ake odyetserako ziweto.+
71 Kuchokera ku banja la hafu ya fuko la Manase, anapatsa anthu a ku banja la Gerisomu mzinda wa Golani+ ku Basana ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Asitaroti ndi malo ake odyetserako ziweto.+