1 Mbiri 6:75 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 75 mzinda wa Hukoki ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Rehobu+ ndi malo ake odyetserako ziweto.
75 mzinda wa Hukoki ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Rehobu+ ndi malo ake odyetserako ziweto.