1 Mbiri 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwana wa Manase,+ yemwe mkazi wake wamngʼono* wa Chisiriya anamʼberekera, anali Asiriyeli. (Mkaziyo anabereka Makiri,+ bambo wa Giliyadi.
14 Mwana wa Manase,+ yemwe mkazi wake wamngʼono* wa Chisiriya anamʼberekera, anali Asiriyeli. (Mkaziyo anabereka Makiri,+ bambo wa Giliyadi.