1 Mbiri 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Makiri anapezera akazi Hupimu ndi Supimu ndipo dzina la mchemwali wake linali Maaka.) Mwana wake wachiwiri anali Tselofekadi,+ koma Tselofekadi anali ndi ana aakazi okhaokha.+
15 Makiri anapezera akazi Hupimu ndi Supimu ndipo dzina la mchemwali wake linali Maaka.) Mwana wake wachiwiri anali Tselofekadi,+ koma Tselofekadi anali ndi ana aakazi okhaokha.+