1 Mbiri 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Ehudi, omwe anali atsogoleri a nyumba za makolo a anthu okhala ku Geba,+ amene anawagwira nʼkupita nawo ku Manahati anali awa:
6 Ana a Ehudi, omwe anali atsogoleri a nyumba za makolo a anthu okhala ku Geba,+ amene anawagwira nʼkupita nawo ku Manahati anali awa: