1 Mbiri 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Beriya ndi Sema. Amenewa anali atsogoleri a nyumba za makolo a anthu okhala ku Aijaloni.+ Iwowa anathamangitsa anthu a ku Gati.
13 Beriya ndi Sema. Amenewa anali atsogoleri a nyumba za makolo a anthu okhala ku Aijaloni.+ Iwowa anathamangitsa anthu a ku Gati.