1 Mbiri 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli onse analembedwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo mʼBuku la Mafumu a Isiraeli. Ndipo Ayuda anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo chifukwa cha kusakhulupirika kwawo.+
9 Aisiraeli onse analembedwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo mʼBuku la Mafumu a Isiraeli. Ndipo Ayuda anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo chifukwa cha kusakhulupirika kwawo.+