-
1 Mbiri 9:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Panalinso Adaya mwana wa Yerohamu. Yerohamu anali mwana wa Pasuri ndipo Pasuri anali mwana wa Malikiya. Komanso panali Maasai mwana wa Adieli. Adieli anali mwana wa Yahazera, Yahazera anali mwana wa Mesulamu, Mesulamu anali mwana wa Mesilemiti ndipo Mesilemiti anali mwana wa Imeri.
-