-
1 Mbiri 9:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Panalinso Salumu mwana wa Kore. Kore anali mwana wa Ebiasafu ndipo Ebiasafu anali mwana wa Kora. Salumu ndi abale ake a kwa bambo ake, mbadwa za Kora, anali oyangʼanira ntchito pochita utumiki wawo ngati alonda apachihema. Makolo awo ankayangʼanira pamsasa wa Yehova ngati alonda apageti.
-