1 Mbiri 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pinihasi+ mwana wa Eliezara+ ndi amene anali mtsogoleri wawo kalekale ndipo Yehova anali naye.