22 Onse amene anasankhidwa kuti akhale alonda apamakomo analipo 212. Iwo ankakhala mʼmidzi yawo mogwirizana ndi mndandanda wa mayina wotsatira makolo awo.+ Davide ndi Samueli wamasomphenya+ anaika anthuwa pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo.