1 Mbiri 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo ndi ana awo ankayangʼanira anthu amene ankachita utumiki wolondera mageti a nyumba ya Yehova kapena kuti chihema chopatulika.+
23 Iwo ndi ana awo ankayangʼanira anthu amene ankachita utumiki wolondera mageti a nyumba ya Yehova kapena kuti chihema chopatulika.+