1 Mbiri 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamagetiwo panali akuluakulu 4 oyangʼanira amene anaikidwa pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo. Iwo anali Alevi ndipo ankayangʼanira zipinda zodyera ndi chuma chamʼnyumba ya Mulungu woona.+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:26 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, ptsa. 9-1012/1/1988, tsa. 21
26 Pamagetiwo panali akuluakulu 4 oyangʼanira amene anaikidwa pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo. Iwo anali Alevi ndipo ankayangʼanira zipinda zodyera ndi chuma chamʼnyumba ya Mulungu woona.+