-
1 Mbiri 9:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Usiku ankakhala mʼmalo awo mozungulira nyumba yonse ya Mulungu woona chifukwa ankachita utumiki wawo waulonda. Iwowa ndi amene ankasunga makiyi nʼkumatsegula nyumbayo mʼmawa uliwonse.
-