1 Mbiri 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ena anasankhidwa kuti aziyangʼanira ufa wosalala,+ vinyo,+ mafuta,+ lubani,*+ mafuta a basamu,+ ziwiya zonse zopatulika+ komanso ziwiya zina.
29 Ena anasankhidwa kuti aziyangʼanira ufa wosalala,+ vinyo,+ mafuta,+ lubani,*+ mafuta a basamu,+ ziwiya zonse zopatulika+ komanso ziwiya zina.