1 Mbiri 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Abale awo ena, mbadwa za Kohati, ankayangʼanira mikate yosanjikiza,*+ kuti aziikonza pa tsiku lililonse la Sabata.+
32 Abale awo ena, mbadwa za Kohati, ankayangʼanira mikate yosanjikiza,*+ kuti aziikonza pa tsiku lililonse la Sabata.+