-
1 Mbiri 10:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Aisiraeli onse amene anali mʼchigwa ataona kuti aliyense wathawa komanso Sauli ndi ana ake afa, anayamba kuthawa mʼmizinda yawo. Kenako Afilisiti anabwera nʼkuyamba kukhala mʼmizindayo.
-