1 Mbiri 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lotsatira, Afilisiti atabwera kudzatenga zinthu za anthu amene anaphedwa, anapeza Sauli ndi ana ake atafa paphiri la Giliboa.+
8 Tsiku lotsatira, Afilisiti atabwera kudzatenga zinthu za anthu amene anaphedwa, anapeza Sauli ndi ana ake atafa paphiri la Giliboa.+