1 Mbiri 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anamuvula Sauli zida zake nʼkumudula mutu. Kenako anauza anthu mʼdziko lonse la Afilisiti kuti afalitse uthengawu kwa mafano awo+ ndiponso kwa anthu onse.
9 Iwo anamuvula Sauli zida zake nʼkumudula mutu. Kenako anauza anthu mʼdziko lonse la Afilisiti kuti afalitse uthengawu kwa mafano awo+ ndiponso kwa anthu onse.