1 Mbiri 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu onse a ku Yabesi+ ku Giliyadi anamva zonse zimene Afilisiti anamuchita Sauli.+