1 Mbiri 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno asilikali onse anapita kukanyamula mtembo wa Sauli ndi mitembo ya ana ake nʼkupita nayo ku Yabesi. Atatero anakwirira mafupa a anthuwo pansi pa mtengo waukulu ku Yabesiko.+ Kenako anasala kudya masiku 7.
12 Ndiyeno asilikali onse anapita kukanyamula mtembo wa Sauli ndi mitembo ya ana ake nʼkupita nayo ku Yabesi. Atatero anakwirira mafupa a anthuwo pansi pa mtengo waukulu ku Yabesiko.+ Kenako anasala kudya masiku 7.