1 Mbiri 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kale Sauli ali mfumu, inuyo ndi amene munkatsogolera Aisiraeli kunkhondo.*+ Ndipo Yehova Mulungu wanu anakuuzani kuti, ‘Udzaweta anthu anga Aisiraeli ndipo udzakhala mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.’”+
2 Kale Sauli ali mfumu, inuyo ndi amene munkatsogolera Aisiraeli kunkhondo.*+ Ndipo Yehova Mulungu wanu anakuuzani kuti, ‘Udzaweta anthu anga Aisiraeli ndipo udzakhala mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.’”+