1 Mbiri 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Davide anati: “Aliyense amene ayambirire kuukira Ayebusi akhala mtsogoleri ndiponso kalonga.” Yowabu+ mwana wa Zeruya ndi amene anayamba kupita, choncho anakhala mtsogoleri.
6 Choncho Davide anati: “Aliyense amene ayambirire kuukira Ayebusi akhala mtsogoleri ndiponso kalonga.” Yowabu+ mwana wa Zeruya ndi amene anayamba kupita, choncho anakhala mtsogoleri.