1 Mbiri 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Otsatirawa ndi amene anali asilikali amphamvu a Davide: Yasobeamu+ mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300 nthawi imodzi.+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:11 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, tsa. 10
11 Otsatirawa ndi amene anali asilikali amphamvu a Davide: Yasobeamu+ mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300 nthawi imodzi.+