1 Mbiri 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anali ndi Davide ku Pasi-damimu+ kumene Afilisiti anasonkhana kuti amenyane nawo. Kumeneko kunali munda wa balere wambiri ndipo anthu anali atathawa chifukwa choopa Afilisitiwo.
13 Iye anali ndi Davide ku Pasi-damimu+ kumene Afilisiti anasonkhana kuti amenyane nawo. Kumeneko kunali munda wa balere wambiri ndipo anthu anali atathawa chifukwa choopa Afilisitiwo.