1 Mbiri 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iye anaima pakati pa mundawo nʼkuuteteza ndipo anapitiriza kupha Afilisiti, moti Yehova anawathandiza kuti apambane.+
14 Koma iye anaima pakati pa mundawo nʼkuuteteza ndipo anapitiriza kupha Afilisiti, moti Yehova anawathandiza kuti apambane.+