1 Mbiri 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako, atatu mwa atsogoleri 30 anapita kwa Davide kuthanthwe, kuphanga la Adulamu.+ Pa nthawiyi asilikali a Afilisiti anali atamanga msasa mʼchigwa cha Arefai.+
15 Kenako, atatu mwa atsogoleri 30 anapita kwa Davide kuthanthwe, kuphanga la Adulamu.+ Pa nthawiyi asilikali a Afilisiti anali atamanga msasa mʼchigwa cha Arefai.+