-
1 Mbiri 11:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Pa nthawi imeneyi nʼkuti Davide ali kumalo ovuta kufikako ndipo asilikali a Afilisiti anali ku Betelehemu.