1 Mbiri 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abisai+ mchimwene wake wa Yowabu+ anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300 ndipo anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:20 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, tsa. 10
20 Abisai+ mchimwene wake wa Yowabu+ anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300 ndipo anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+