1 Mbiri 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kwambiri kuposa amuna 30 aja, sankafanana ndi amuna atatu aja.+ Koma Davide anamuika kukhala mmodzi wa asilikali ake omulondera.
25 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kwambiri kuposa amuna 30 aja, sankafanana ndi amuna atatu aja.+ Koma Davide anamuika kukhala mmodzi wa asilikali ake omulondera.