1 Mbiri 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsiku lililonse anthu ankabwera kwa Davide+ kudzamuthandiza, mpaka anachuluka nʼkukhala gulu lalikulu lankhondo, ngati gulu lankhondo la Mulungu.+
22 Tsiku lililonse anthu ankabwera kwa Davide+ kudzamuthandiza, mpaka anachuluka nʼkukhala gulu lalikulu lankhondo, ngati gulu lankhondo la Mulungu.+