1 Mbiri 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Awa ndi manambala a atsogoleri a anthu okonzekera kumenya nkhondo amene anabwera kwa Davide ku Heburoni,+ kudzamʼpatsa ufumu wa Sauli mogwirizana ndi lamulo la Yehova.+
23 Awa ndi manambala a atsogoleri a anthu okonzekera kumenya nkhondo amene anabwera kwa Davide ku Heburoni,+ kudzamʼpatsa ufumu wa Sauli mogwirizana ndi lamulo la Yehova.+