-
1 Mbiri 12:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 A fuko la Zebuloni, analipo 50,000, okonzeka kumenya nkhondo ndipo anali ndi zida zonse zomenyera nkhondo. Onsewa anapita kwa Davide ndipo sanapite ndi mtima wachinyengo.
-