1 Mbiri 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kutsidya lina la Yorodano+ kunachokera asilikali a fuko la Rubeni, a fuko la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase okwana 120,000, okhala ndi zida zonse zankhondo.
37 Kutsidya lina la Yorodano+ kunachokera asilikali a fuko la Rubeni, a fuko la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase okwana 120,000, okhala ndi zida zonse zankhondo.