1 Mbiri 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Davide anakambirana ndi atsogoleri a anthu 1,000 ndi a anthu 100 ndiponso mtsogoleri aliyense.+