-
1 Mbiri 13:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Koma atafika kumalo opunthira mbewu a Kidoni, Uza anatambasula dzanja lake nʼkugwira Likasalo, chifukwa ngʼombe zinatsala pangʼono kuligwetsa.
-