1 Mbiri 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Davide sanatenge Likasalo kupita nalo kumene ankakhala, ku Mzinda wa Davide. Mʼmalomwake iye analamula kuti lipite kunyumba ya Obedi-edomu wa ku Gati.*
13 Davide sanatenge Likasalo kupita nalo kumene ankakhala, ku Mzinda wa Davide. Mʼmalomwake iye analamula kuti lipite kunyumba ya Obedi-edomu wa ku Gati.*