1 Mbiri 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ popeza ufumu wakewo unakwezedwa kwambiri chifukwa cha anthu a Mulungu, Aisiraeli.+
2 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ popeza ufumu wakewo unakwezedwa kwambiri chifukwa cha anthu a Mulungu, Aisiraeli.+