1 Mbiri 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Mulungu kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi mukawapereka mʼmanja mwanga?” Yehova anauza Davide kuti: “Pita, amenewa ndiwaperekadi mʼmanja mwako.”+
10 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Mulungu kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi mukawapereka mʼmanja mwanga?” Yehova anauza Davide kuti: “Pita, amenewa ndiwaperekadi mʼmanja mwako.”+